Kupanga ming’oma yamakono

Kudzera munjira yakale, njuchi zimapanga zokha malesa omwe amakhala ophatikana, kotero kukolola kumakhala kovuta. Munjira yamakono, uchi amapakula pogwiritsa ntchito chipangizo chopakulira uchi. Uchi umapakulidwa posaononga zitsa. Zisa zopanga kanthu amazibwenzeretsa kuti njuchi zikayikemo  uchi wina, kotero kuthandiza njuchi kusataya nthawi ndi mphamvu kukonzanso kapena kubwenzeretsa zitsa.

Current language
Chichewa / Nyanja
Need a language?
If you would like this video translated into other languages, please contact kevin@accessagriculture.org
Uploaded
3 years ago
Duration
15:30
Produced by
Practical Action Nepal