Kudzala udzu poteteza kukokoloka kwa nthaka

Udzu odzalidwa mmigwere umachepetsa liwiro lamadzi ndipo amalowa mnthaka. Migwere imagwiranso dothi lokokoloka ndikusunga michere yake mnchimake. Mutha kudzala udzu osiyanasiyana kutengera ndi zomwe mukufuna komanso kupezekeratu kwa udzu mosavuta.

Current language
Chichewa / Nyanja
Need a language?
If you would like this video translated into other languages, please contact kevin@accessagriculture.org
Translated in
Malawi
Translation funded by
GIZ
Uploaded
2 years ago
Duration
12:20
Produced by
Agro-Insight