Chuma mu Uchi

Kale, uchi unkagulitsidwa ndi malesa omwe osafinya, koma masiku ano makasitomala amafuna uchi omwe wakonzedwa bwino. Uchi omwe okonzedwa ndiwaukhondo komanso utha kusungidwa kwa nthawi yayitali. Kuti uchi ukhale wabwino, muyenera kutsatila ngodya zitatu izi: koyamba, fulani uchi okhawo omwe wakhwima, kachiwiwri, Khalani awukhondo pamene mukufula komanso kukonza uchi, kachitatu, onetsetsani kuti ziwiya zonse komanso mabotolo ndizosamalidwa ndikuwuma bwino.

Current language
Chichewa / Nyanja
Need a language?
If you would like this video translated into other languages, please contact kevin@accessagriculture.org
Uploaded
7 years ago
Duration
11:00
Produced by
NASFAM, NOGAMU, Egerton University, ATC/UNIDO