<<90000000>> viewers
<<320>> entrepreneurs in 18 countries
<<5432>> agroecology videos
<<110>> languages available

Zitsamba zothamangitsira tizilombo

Uploaded 1 month ago | Loading

Pachikhalidwe chake, zomera zina zimathamangitsa tizirombo. Dzalani zimenezo mminda yanu. Podziwa zitsamba zomwe zimamera mdera lanu, mutha kupanga mankhwala opilikitsira tizirombo popanda kuononga ndalama iliyonse. Onjezerani mkodzo wa ng’ombe kuzitsambazi kuti zitulutse mwachangu timankhwala tothamangitsa tizirombo toononga. Ndibwino kukhala ndi mitundu iwiri yamankhwala kuti muzisinthasintha. Konzani mtundu wina wa mankhwala pogwiritsa ntchito chiphala cha ginger, garlic ndi tsobola.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Green Adjuvants
Share this video:

With thanks to our financial partners