Kubwezeretsa chonde mnthaka pokwiliramo mbewu zobiliwira
Uploaded 2 months ago | Loading

14:29
tundu wa mbeu iliyonse ndi masamba a mitengo zili ndi mlingo wake obweretsa chonde ndi tizilombo tofunikira mmunda.Izi zimaonjezera zowolerana ndi kuchulukitsa tizilombo tofunikira mnthaka komanso kubwenzeretsa chonde
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Shanmuga Priya J.