Kukonza chimera chodyetsera ziweto
Uploaded 1 month ago | Loading

14:58
Reference book
Mbeu zikanyikidwa ndikuzisiya kuti zimele, zimatulutsa timitima. Chifukwa chakumwa madzi, mbeuzi zimalemera kwambiri. Chimera sichivuta kugaika ng’ombe ikadya kuyerekeza ndi chimanga. Chimera ndi chakudya chabwino. Chimera chili ndi michere yomwe imathandizira kugaika ziweto zikadya. Chimera chimakhala ndimichere yochuluka monga ma vitamin.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Atul Pagar, Govind Foundation