Kukonza zakudya za ziweto zosaboola mthumba
Uploaded 1 month ago | Loading

10:20
Reference book
- English
- Arabic
- Bangla
- French
- Hindi
- Spanish
- Ateso
- Baoulé
- Bariba
- Bisaya / Cebuano
- Burmese
- Chichewa / Nyanja
- Chitonga / Tonga
- Dholuo
- Fon
- Fulfulde (Cameroon)
- Hausa
- Hiligaynon
- Kannada
- Kanuri / Kanouri
- Kikongo / Kongo
- Kikuyu
- Kiswahili
- Lingala
- Maninka / Eastern Maninkakan
- Marathi
- Sinhala
- Tagalog
- Tamil
- Telugu
- Tshiluba / Luba-Lulua
- Twi
- Yoruba
Popanga ufa oyambira omwe ziweto zonse zitha kudya, mmapulumutsa nthawi ndi ndalama. Posakaniza mbeu, magawo awiri mwa magawo atatu ndi a mbeu za mgulu la chimanga : monga mapira, chimanga ndi mpunga. Gawo limodzi la magawo atatu azakudyazi, limakonzedwa ndi mbeu zomanga thupi komanso gawo la zamafuta. Gayitsani ufa wamisere pokonza chakudya choyambira. Kutengera ndi mtundu wa ziweto, mutha kumaonjezera zipangizo zina.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
AIS, MSSRF, WOTR