Kukwatitsa mbande za mango
Uploaded 2 months ago | Loading

15:25
Reference book
Ndi njira yokwatitsa mitengo, nthambi yamango omwe tikuwafuna timaiphatika ku mbande. Mbandeyi imasanduka thundi ndi mizu. Ichitu ndi chitsindetsinde cha mtengo okwatitsawu. Kanthambi komwe timakatenga kumtengo wina ndikudzakwatitsa kumbande ndikomwe kamadzakula kukhala mtengo.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Practical Action, Bangladesh and Nepal, Christian Commission for Development in Bangladesh (CCDB)