Kupha ntchentche za mzipatso pogwritista ntchito nyambo
Uploaded 2 months ago | Loading

11:36
Nyambo za zakudyazi zitha kugwiritsidwa ntchito popopera mmalo osiyana-siyana, kapena kuziika mmalo okhazikika. Ntchentche za mzipatso zimazindikira nyambozi zikaziwandikira mwina pa mtunda wa mamita 10. Nyambo zina zimakhala ndi mankhwala ophera tizirombo achilengedwe omwe ndi ololedwa.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight