Kuphimbira nthaka ndi mitengo komanso zitsamba kuti mbeu zikule bwino
Uploaded 1 month ago | Loading

12:58
Kuphimbira nthaka ndi mitengo komanso mphukira kumateteza dothi ku dzuwa ndikuziziritsa mpweya, zomwe ndizofunika ku zamoyo zopezeka mu dothi. Dulani mphukira mosamala kuti zotsalazo zitha kuphukiranso ndikukula mosavuta. Phimbirani munda wanu sabata imodzi kapena ziwiri musadadzale. Mukamadzala, kankhani zophimbira pang’ono ndikuboola bowo lodzalapo mbeu.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Access Agriculture