Mavu oteteza mbewu zathu
Uploaded 3 months ago | Loading

8:29
Posunga mipanda yamitengo yamoyo ndi zomera zachilengedwe zamaluwa mozungulira munda wanu, mumathandiza kuteteza mavu ndi tizilombo tina tofunikira. Komanso ndizotheka kulima Kinoya popanda kupopera mankhwala, kwinaku mukuteteza nthaka yanu.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight, PROINPA