<<90000000>> viewers
<<320>> entrepreneurs in 18 countries
<<5432>> agroecology videos
<<110>> languages available

Momwe mungagulitsire zakudya kapena zokolora zosalimira mankhwala

Uploaded 1 month ago | Loading

Mukamagulitsa mmalo azionetsero, mutha kukhala ndi chizindikiro chimodzi ngati gulu, mwachitsanso kugwiritsa msalu zoyala pa magome zofanana. Konzani njira zophunzitsira ogula komanso ana awo. Pangani maubale ndi akuluakulu aboma kuti mukonze malo ogulitsira mbeu zamtunduwu mosiyanitsa ndi zomwe amalimira mankhwala.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight
Share this video:

With thanks to our financial partners