Mthilira ogwiritsa ntchito Mitsuko
Uploaded 1 month ago | Loading

13:24
Ndi mthilira wa mitsuko, alimi amakwirira mitsuko yatimabowo pafupi ndi mbewu zawo, ndikuthira madzi mmitsukomo. Madzi amatuluka pang’ono pang’ono kukafika ku mizu ya mbeu zathu podzera mtimabowo tamitsukoyi. Pomwe mbeuzi zikugwiritsa ntchito madziwa, miphikayi imapitilira kutulutsa madzi. Izitu zikutanthauza kuti, mtsuko umatulutsa madzi okhawo omwe akufunikira ku mbeu zathu.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Green Adjuvants