<<90000000>> viewers
<<320>> entrepreneurs in 18 countries
<<5432>> agroecology videos
<<110>> languages available

Kusunga ndondomeko ya ulimi wakasakaniza

Uploaded 1 month ago | Loading

Pamene mitundu ya ulimi ikuchuluka pa munda, zimakhala zovuta kusunga ndondomeko ya zomwe zikulowa komanso kutuluka. Pamene zochita zikuchuluka pa ulimi wanu, mukuyenera kusunga kalembera wa zochitika. Pamen mukufanizira kalembera wanu ndi alimi ena, mutha kudziwa ngati pali pofunika kusintha. Pena mutha kuwona ngati ulimi wakasakaniza ndiwovuta koma kalembera amene tawona akusonyeza kuti mumakhala phindu lochuluka kuposera kasanu ndipo mumakhala ndi chakudya nthawi zonse.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
PPA, Alangilan National High School, NISARD
Share this video:

With thanks to our financial partners