Kuona umoyo wa m’dothi
Uploaded 1 month ago | Loading

9:20
Zamoyo zambiri zikamapezeka mu dothi, zimatanthauza kuti dothilo ndilamoyo chifukwa tizilomboti timathandiza kuwoletsa zotsalira mmunda ndikuthandizira kupezeka kwa chakudya cha mbeu komanso kufewetsa dothi.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight