Tisunge chimanga chathu moyenera
Uploaded 2 months ago | Loading

7:35
Chimanga chidzikhala chouma bwino ndi chaukhondo musanachisunge. Chimanga chimakhala chotetezeka ku tizilombo ndi matenda kwa nthawi yaitali munkhokwe yachitsuro, ngati mwachisunga moyenera.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
TV Agro-CentroAmerica