Kupha mbozi zooneka ngati ntchembere zandonda pogwiritsa ntchito njira zachilengedwe

Ngati mukukwanitsa kugwiritsa ntchito abwenzi a mlimi komanso mankhwala ochokera ku zinthu zachilengedwe, mudzawona kuti mukukwanits kuthana ndi vuto la mbozi zooneka ngati tchembere zandona ndi kupeza zokolola zochuluka

Current language
Chichewa / Nyanja
Need a language?
If you would like this video translated into other languages, please contact kevin@accessagriculture.org
Translated in
Malawi
Uploaded
4 years ago
Duration
15:40
Produced by
Agro-Insight and FAO