Kusamalira nkhuku zachikuda

Yikani utuchi ndi udzu ouma kuti nkhuku isavutike poikira madzira.Izi zimachepetsa chinyezi komanso kuchepetsa matenda. Palinso mavuto ena kupatula pa tizilomboti. Sabata zoyambilira, anapiye amatsekeredwa mkhola poziteteza ku zilombo zina komanso kuti zisasowe. Mu kanema uyu, ationetsa njira zosavuta, zosalira ndalama kuti mukhale ndi nkhuku za thanzi.

Current language
Chichewa / Nyanja
Need a language?
If you would like this video translated into other languages, please contact kevin@accessagriculture.org
Translation funded by
GIZ
Uploaded
2 years ago
Duration
10:12
Produced by
NASFAM, NOGAMU, Egerton University, ATC/UNIDO, Songhaï Centre