Kuphimbira nthaka ndikothandiza kuti mbewu zichite bwino

Mutha kuphimbira ndi zinthu zambiri ngati udzu, masangwi kapena masamba.Kuphimbira ndikophweka. Kumathandiza kusunga chinyontho, nthawi ndi kuchepetsa ntchito, kwinaku mukuonjezera chonde mnthaka komanso mukukolola zochuluka.

Current language
Chichewa / Nyanja
Need a language?
If you would like this video translated into other languages, please contact kevin@accessagriculture.org
Translated in
Malawi
Translation funded by
GIZ
Uploaded
2 years ago
Duration
11:35
Produced by
Atul Pagar, WOTR