Kulima tomato mopatsana mpata

Kumadera akumadzulo kwa Africa, anthu amakonda kugwiritsa ntchito tomato mu zakudya zawo. Mu ulimi wa tomato, musamangolima poti aliyense akulima basi, mutha kudzakhumudwa chifukwa cha kutsika mtengo. Kulima kopatsana mpata kumathandiza kuti tomato asasowe pamsika.

Current language
Chichewa / Nyanja
Need a language?
If you would like this video translated into other languages, please contact kevin@accessagriculture.org
Translated in
Malawi
Translation funded by
GIZ
Uploaded
2 years ago
Duration
5:56
Produced by
Countrywise Communication