Kupanga mankwala kuchokera ku njere za Nimu

Kusiyana ndi mankhwala ena achilengedwe, mbewu imamwa madzi a nimu kupyolera ku mizu ndi masamba ndi kufarikira ku mtengo onse.Choncho, nimu amathandiza kuthana ndi tizirombo monga mbozi zomwe zimadya masamba, zimene  nthawi zambiri sizifa ndimankhwala ena.

Current language
Chichewa / Nyanja
Need a language?
If you would like this video translated into other languages, please contact kevin@accessagriculture.org
Translated in
Malawi
Translation funded by
GIZ
Uploaded
2 years ago
Duration
15:11
Produced by
Atul Pagar, WOTR