Kuthana ndi akodikodi amu chinangwa

Alimu aku Thailand akuwonetsa njira zothandiza kuti akodikodi asafike mmunda wanu wachinangwa. Chidwi chalunjika ku nthawi yodzalira; kudzala mbeu zathanzi; kukonza mbewu kuti muphe tizilombo; kuteteza tizilombo tofunika; ndi kukhala ndi chidwi ndi mbeu zanu. Dziwani: mukanema uyu muli pena ndi pena pomwe mankhwala ophera tizilombo akambidwa.

Current language
Chichewa / Nyanja
Need a language?
If you would like this video translated into other languages, please contact kevin@accessagriculture.org
Translation funded by
FRI
Uploaded
1 month ago
Duration
15:22
Produced by
Agro-Insight