Kupelekera zakudya zolimidwa popanda mankhwala aliwonse, pakhomo lawogula

Alimi amatsatsa mbewu zolimidwa mosagwiritsa ntchito feteleza kapena mankhwala ena aliwonse pamakina a internet ndipo ogula amawoda katunduyu kuyambira pa theka kufika 5 kgs. Ogula amalandira chakudya chopatsa thanzi pakhomo pawo. Pokhala ndi makasitomala odziwikiratu, alimi amapeza ndalama pafupi-fupi ndipo amagulitsa katundu wawo pamitengo yokwerelapo.

Current language
Chichewa / Nyanja
Need a language?
If you would like this video translated into other languages, please contact kevin@accessagriculture.org
Translated in
MALAWI
Translation funded by
GIZ - KCOA
Uploaded
4 months ago
Duration
15:19
Produced by
Atul Pagar