Kupitasa patsogolo ulimi ndi Njele zabwino
Tiyeni tione alimi a mudzi wa Nkungi a dera la pakati dziko la Tanzania mene anayesera mbewu zamakono pa munda wawo ophunzilira za malimidwe. Bvuto lalikulu linali lopeza ntundu wa mapila omwe sumagwindwa kwambiri ndi kaufiti.
Current language
Chichewa / Nyanja
Available languages
Need a language?
If you would like this video translated into other languages, please contact kevin@accessagriculture.org
Uploaded
6 years ago
Duration
10:53
Produced by
Agro-Insight, ICRISAT