Kusunga ndi kusamala chimanga mnyumba yosungiramo
Uploaded 5 years ago | Loading
13:02
Tsatirani njira izi pofuna kusunga ndi kusamala mbewu mu nyumba yosungilamo . njirazi nazi :Choyamba, konzani nyumba yosungiramo ;Kachiwiri, ikani mbewu zanu pa mitengo ;Kachitatu mudziyendera ndi kusamala mbewu zanu munyumbazi.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Songhai and Helvetas