Mankhwala azisamba othana ndi masaitisi
Uploaded 3 years ago | Loading
15:12
Mastitis ndi nthenda yodziwika ya ng’ombe za mkaka. Tizilombo tikalowa mitsempha ya bele, timabelekana ndikuyambitsa matenda. Bele limalimba ndi kutupa. Ngati nthendayi siinachizike ikhoza kuononga bele. Ngati ng’ombe yagwidwa ndi nthenda ya mastitis, mkaka wake siwabwino kumwa.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Atul Pagar, Anthra