SLM00 Njira zodalirika zosamalira nthaka
Uploaded 1 year ago | Loading
7:28
Chiyambi cha njira zosamalira nthaka, zomwe zayesedwa mu Africa. Njirazi zitha kuthandiza kuchepetsa kuonongeka kwa nthaka ndi kuchulukitsa phindu kwa alimi ang'onoang'ono, ngakhale pali mavuto a kusintha kwanyengo.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Countrywise Communication, CIS Vrije Universiteit Amsterdam