<<90000000>> viewers
<<266>> entrepreneurs in 18 countries
<<4647>> agroecology videos
<<107>> languages available

SLM06 Kudzala mbewu m’mayenje a Zaï

Uploaded 2 years ago | Loading

Mayenje a Zaï, monga amadziwikira ku Burkina Faso, kapena tassa ku Niger ndi maenje odzala mbewu, otambalala. Amakhala ngati misampha ndipo atha kugwiritsidwa ntchito kubwenzeretsa chonde munthaka mukamagwitsa ntchito limodzi ndi manyowa. Akhala ali opambana kumadzuro kwa Africa mu zaka 25 zapitazo.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Countrywise Communication, CIS Vrije Universiteit Amsterdam
Share this video:

With thanks to our financial partners