SLM01 Mizere ya miyala
Uploaded 4 years ago | Loading
7:35
Reference book
Mudzaka za mma 1970 muchipululu chaku Sahel, ng’amba inawononga nthaka ndi kubweretsa mavuto. Mabanja ena anaganiza zongosamuka.Ngakhale Mvula ikugwa, madzi amangothamanga ndi kukokolola chonde.Koma mwayi unalipo oti akanatha kuyala miyala mumizere pamwamba pa akalozera ndi kuchepetsa kuthamanga kwa madzi. Alimi ochepa anakwanitsa kuchita izi.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Countrywise Communication, CIS Vrije Universiteit Amsterdam