Kulima azolla chakudya cha ziweto
Uploaded 2 years ago | Loading
![](https://accessagfiles-drupal9-download.s3.eu-west-1.amazonaws.com/attachments/2016-10/Azolla.jpg?VersionId=66h2gam7MJUvQuMfHLp.smBw2s1pk3Jo)
13:10
Azolla amapanga yekha nitrogen kuchokera mu mpweya ndikumusunga mmasamba ake. Azolla ali ndi maprotini, ma vitamini ndi michere yochuluka kuposa mbewu ndi zomera zobiliwira zambiri. Chifukwa cha izi komanso kuti amakura nsanga, ngakhale pamalo ochepa, azolla ndi chakudya chaziweto choonjezera chabwino.Azolla amapanga yekha nitrogen kuchokera mu mpweya ndikumusunga mmasamba ake. Azolla ali ndi maprotini, ma vitamini ndi michere yochuluka kuposa mbewu ndi zomera zobiliwira zambiri. Chifukwa cha izi komanso kuti amakura nsanga, ngakhale pamalo ochepa, azolla ndi chakudya chaziweto choonjezera chabwino.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
AIS, MSSRF, WOTR