Kupanga manyowa a madzi okulitsa mbewu
Uploaded 1 year ago | Loading
15:49
Mutha kupanga manyowa othandizira mbewu kukula pogwiritsa ntchito zinthu zopezeka panyumba, monga ndowe, chambiko, mkaka, mkodzo, shuga ndi nthochi zakupsa. Kuti manyowawa akhale a mphamvu, mutha kuwonjezera nkodzo kapena zisamba zina zonunkhira kuti zithandizire kuteteza mbewu ku tizirombo ndi matenda osiyana-siyana.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
MSSRF