Kukutira mbewu za mgulu la chimanga mmanyowa
Uploaded 1 year ago | Loading
12:16
Chikuto cha manyowa chimateteza mbewu ku mbalame ndi tizirombo ndipo zimapereka chinyontho ku njere komanso kuwonjezera michere yofunikira ku mbewu. Muthanso kudzala mbewu yokutilidwa mwachangu, mvula isanayambe.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Access Agriculture, IVTSANE