Kuthana ndi matenda a chiwawu mu mpunga
Uploaded 4 years ago | Loading

13:00
Reference book
Matendewa atha kukhudza mbeu ku nazale kapena kumunda. Nazare siyichedwa kuwuma maka ngati yagwidwa mopyola muyezo. Matendewa amawonekera msanga kunsonga kwa masamba.Matendawa amayamba ngati madontho kenaka nkumafalikila kutsamba lonse.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
MSSRF