Njira zothana ndi ntchentche zamuzipatso
Uploaded 2 years ago | Loading
12:52
Reference book
- English
- Arabic
- Bangla
- French
- Hindi
- Portuguese
- Spanish
- Assamese
- Ateso
- Bambara
- Bariba
- Bisaya / Cebuano
- Chichewa / Nyanja
- Chitonga / Tonga
- Dioula
- Fon
- Ghomala
- Hiligaynon
- Kiswahili
- Kriol / Creole (Guinea-Bissau)
- Luganda
- Malagasy
- Marathi
- Mooré
- Persian / Farsi
- Peulh / Fulfuldé / Pulaar
- Tagalog
- Telugu
- Tumbuka
- Wolof
- Yao
Ntchentche zamuzipatso zimayikira mazira ake mu zipatso. Ntchenthe imodzi ikhoza kuyikira mazira zikwi zingapo, amene amazasanduka mphutsi zimene zimadya chipatso mkati. Ngati simuchitapo kanthu mwansanga, zipatso zanu zitha kuwonongeka. Nthawi zonse phatikizani njira zingapo monga misampha, nyambo, kulimbikitsa nyerere zofira mmunda, komanso kukwilira zipatso zimene zagwa pansi, kut muthane ndi ntchentche zofirazi.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight