<<90000000>> viewers
<<266>> entrepreneurs in 18 countries
<<4647>> agroecology videos
<<107>> languages available

Bank Ya Kumudzi

Uploaded 6 years ago | Loading

Bank ya kumudzi imathandiza abambo, amayi ndi achinyamata kusunga ndalama posadalira mabank akuluakulu. Tikamasunga ndalama ngati gulu, timathandizira kuti ntchito zamalonda zipite patsogolo komanso kuthandizana wina ndi mnzake kumudzi.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Ronald Udedi
Share this video:

With thanks to our financial partners