Kuonetsetsa kuti ulimi ochulukitsa akalulu ukupindulitsa
Uploaded 2 years ago | Loading

11:39
Mukanema uyu tiona mmene tingapangire kalondolondo pa ulimi wathu wa akalulu. Polembera kaundura ndi kusunga lipoti lazachuma titha kukhala ndi ulimi opambana, komanso opindulitsa.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Songhai Centre