Kupewa matenda mu ulimi wa akalulu
Uploaded 2 years ago | Loading

14:38
Coccidiosis ndi colibacillosis ndi matenda oopsya mu akalulu chifukwa ndiopatsirana. Mankhwala akusitolo samatha kuchiziratu matendawa. Komatu mwamwayi, matendawa ndiopeweka, mmene tionere mu kanema uyu.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Songhai Centre