Bizinesi yoweta anapiye a Nkhuku pakhomo
Uploaded 2 years ago | Loading
10:39
Mukanemayu, tiyendera amai oweta anapiye adela la Fayoum, mdziko la Egypt ndipo tiphunzira ndondomeko zabwino zothandiza pa bizinesi yoweta anapiye a nkhuku.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Nawaya, UNIDO Egypt