<<90000000>> viewers
<<266>> entrepreneurs in 18 countries
<<4647>> agroecology videos
<<107>> languages available

Kuchulukitsa Nkhuku Zalokolo

Uploaded 2 years ago | Loading

Kawirikawiri, nkhuku zalokolo zimaswa anapiye ochepa pazifukwa. Kuti mukhale ndi mazira komanso amapiye ambiri, pali njira zosavuta zomwe mukhonza kutsatira. Pokhala ndi nkhuku zalokolo zambiri komanso zathanzi, mutha kudyetsa banja lanu ndi kupha makwacha.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Practical Action
Share this video:

With thanks to our sponsors