Njira zachilengedwe zothandiza nkhuku kukhala zathanzi
Uploaded 2 years ago | Loading
13:40
Reference book
Madzi okumwa akuda, malo osasamalika ndi chakudya chosalongosoka zimabweletsa matenda pa nkhuku. Samalani mukhola ndikuchotsa zitosi komansobchakudya choononheka tsiku ndi tsiku. Iphani majelemusi mmadzi posakanizamo turmeric kapena potassium permanganate. Zipatseni nkhuku chakudya chopatsa thanzi. Onjezerani Adyo kapena anyezi muchakudya cha nkhuku kuti zikhale zathanzi. Masamba a zomera zonyung'unya amathandiza kupewa tizilombo. Pewani kuchepa kwa calcium pozipatsa nkhuku lime kapena makoko amazira. Mangani kampukutu ka masamba akafungo ndikumangilira mukhola la nkhuku ndipo tizilombo timathawa.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Atul Pagar, ANTHRA