Kuchulukitsa Akalulu
Uploaded 1 year ago | Loading
13:00
Ndikofunikira kutsatira njira zabwino poweta akalulu kuti adziswa bwino, chifukwa pali phindu lochuluka. Mukatsata njira zabwino, akalulu anu akazi amakhala athanzi ndipo amaswa ana ochuluka omwenso atha kugulitsidwa pamtengo wabwino.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Songhai