Kusunga mbatatesi mu utuchi
Uploaded 3 years ago | Loading
8:42
Koma alimi ambiri alibe magetsi komanso filiji zimenezi. Kotero, alimi ena amasunga mbatatesi zawo mu udzu. Koma alimi ena amagwiritsa ntchito utuchi kuti asunge kachewere kwa miyezi isanu ndi umodzi.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Biovision