<<90000000>> viewers
<<240>> entrepreneurs in 17 countries
<<4135>> agroecology videos
<<105>> languages available

Akalozera

Uploaded 3 years ago | Loading

Mmadera aku anyengo yo uma a Savana, mvula imagwa yochepa komanso ndiyo sidalilika, ndipo kupeza njira zothandiza kugwira madzi kumapangitsa mlimi kukolola zocholuka kapena zochepa.Mukhoza kuchepetsa liwiro lamadzi popanga akalozera.Akalozera ndimizere yokhazikika yomwe kukula kwake imapangidwa mofanana.Kwa zaka makumi awiri, alimi aku Burkina Faso ndi Mali akhala akupanga akalozera mminda yawo, maka mmalo okwera.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight
Share this video:

Related Videos

How you can help... Your generous donation will enable us to give smallholder farmers better access to agricultural advice in their language.

With thanks to our sponsors