<<90000000>> viewers
<<240>> entrepreneurs in 17 countries
<<4135>> agroecology videos
<<105>> languages available

Kudzala, kupatula ndi kuwonekera mapira

Uploaded 3 years ago | Loading

Kudzala zambiri komanso kuchepetsa mizere ndi kudzala  pa mlingo oyenera mumapando ndi chiyambi chokhala ndi mbeu yokula mofanana ndi kukolola zochuluka.Mbali ina ngati  mudzala mbeu mofupikana, zimalephera kukula bwino. Mbeu zimakhala zowonda ndipo sizichedwa kugwidwa ndi matenda ndi tizilombo monga udzu wa kaufiti. Mu kanema uyu, tiphunzira kudzala mlingo oyenera wa mapira. Tiphunzira zithu zomwe zimathandiza mbeu kukula pamalo komaso mmene  kupatula ndi kuwokera kungathandizire mbeu kukula mofanana ndi kubereka kwambiri.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
ICRISAT, MOBIOM
Share this video:
How you can help... Your generous donation will enable us to give smallholder farmers better access to agricultural advice in their language.

With thanks to our sponsors