<<90000000>> viewers
<<240>> entrepreneurs in 17 countries
<<4135>> agroecology videos
<<105>> languages available

Njila zosakaniza zogonjetsera Kaufiti

Uploaded 8 years ago | Loading

Mukanemayu tiona za udzu wa kaufiti omwe ndi owononga kwambiri komaso umagwira mbewu zagulu la mapila. Timphunzira njira zosiyanasiyana zotetezera udzuwu ku mbewu ndi njira zomwe tingagonjetsere m’daniyu. Kodi tingachite chiyani? Njila yake ndi kusakaniza njira zogonjetsera kaufiti komaso kusamala chonde mu nthaka.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight, ICRISAT, UACT
Share this video:
How you can help... Your generous donation will enable us to give smallholder farmers better access to agricultural advice in their language.

With thanks to our sponsors