Kukolora chinangwa kwaphweka
Uploaded 3 years ago | Loading
10:00
Onetsetsani kuti nthaka yanu ndiyachonde ndipo dzalani mbewu zamuguru lanyemba mmunda wanu wachinangwa kuti nthaka ikhake yofewa. Dzalani chinangwa chanu mopendeketsa kuti chiike pafupi. Ndi chipangizo chamakono mutha kukolora mwachangu pogwiritsa ncthito theka la nthawi yomwe munakatenga pozula ndimanja
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight