Kuthana ndi akodikodi amu chinangwa
Uploaded 3 years ago | Loading
10:49
Reference book
Alimu aku Thailand akuwonetsa njira zothandiza kuti akodikodi asafike mmunda wanu wachinangwa. Chidwi chalunjika ku nthawi yodzalira; kudzala mbeu zathanzi; kukonza mbewu kuti muphe tizilombo; kuteteza tizilombo tofunika; ndi kukhala ndi chidwi ndi mbeu zanu.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight