Kupanga zakudya zokhwasula Kuchokera ku chinangwa
Uploaded 2 years ago | Loading
16:53
Chinagwa chabwino chimakhala chaukhondo, chonunkhira bwino ndi choyera mkati mukachidura. Chinangwa chosasawa chimakoma. Mukamagwiritsa ntchito chinangwa chowawa, mudziyamba kuchiviika kaye kwa masiku atatu, kuchotsa zowawa zonse, kenaka muchitsuke.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Musdalafa Lyaga