Kusamalira ana akalulu
Uploaded 2 years ago | Loading
11:00
Kalulu akaswa, amayenera kusamalidwa bwino. Pamafunika kukonza malo abwino a ana komanso thaziyo amayenera kupatsidwa mpata oti abweleremo asanatengenso bele.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Songhaï Centre