Mbewu yabwnio ya chinangwa
Uploaded 3 years ago | Loading
15:40
Reference book
Nthaka ya chonde imatulutsa mbewu yabwino. Konzani munda wanu munthawi yabwino. Dzalani mbewu ya chinangwa mukangotchola, isanaume.Kumbukirani kuti mukadzala mbewu yabwino yachinangwa, ndiye kuti mudzakololanso chinangwa chabwino.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight